2 Tsopano ndikufotokozera choonadi:+
“Mu ufumu wa Perisiya+ mudzauka mafumu atatu, ndipo mfumu yachinayi+ idzasonkhanitsa chuma chambiri kuposa ena onsewa.+ Ndipo ikadzangokhala yamphamvu chifukwa cha chuma chakecho idzaukira ufumu wa Girisi ndi mphamvu zake zonse.+