Hoseya 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+ Amosi 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Malo okwezeka a Isaki+ adzawonongedwa, ndipo malo opatulika+ a Isiraeli nawonso adzasakazidwa.+ Ine ndidzaukira nyumba ya Yerobowamu* ndi lupanga.”+
15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+
9 Malo okwezeka a Isaki+ adzawonongedwa, ndipo malo opatulika+ a Isiraeli nawonso adzasakazidwa.+ Ine ndidzaukira nyumba ya Yerobowamu* ndi lupanga.”+