Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno mfumu ya ana a Amoni inauza amithenga a Yefita kuti: “N’chifukwa chakuti Aisiraeli analanda dziko langa atatuluka mu Iguputo.+ Analanda dzikoli kuyambira ku Arinoni+ mpaka ku Yaboki ndi kukafikanso ku Yorodano.+ Tsopano undibwezere dzikoli mwamtendere.”

  • Yeremiya 49:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ponena za ana a Amoni+ Yehova wanena kuti: “Kodi Isiraeli alibe ana aamuna, kapena kodi alibe wolandira cholowa? N’chifukwa chiyani Malikamu+ watenga Gadi+ kukhala cholowa chake? N’chifukwa chiyani anthu olambira Malikamu akukhala m’mizinda ya Isiraeli?”+

  • Ezekieli 35:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Iwe unanena kuti, ‘Mitundu iwiri iyi ya anthu ndi mayiko awiri awa zidzakhala zanga ndipo ife tidzatenga mayiko awiri onsewo.’+ Unanena zimenezi ngakhale kuti Yehova anali komweko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena