Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano mwamuna wina anali kukhala ku Maoni,+ koma ntchito yake anali kugwirira ku Karimeli.*+ Mwamuna ameneyu anali wotchuka kwambiri, ndipo anali ndi nkhosa 3,000 ndi mbuzi 1,000. Tsiku lina, iye anali kugwira ntchito yometa ubweya+ wa nkhosa zake ku Karimeli.

  • Yesaya 33:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Dzikolo likulira, lafota.+ Lebanoni wachita manyazi, wanyala.+ Sharoni+ wakhala ngati chipululu ndipo Basana ndi Karimeli akuyoyola masamba awo.+

  • Nahumu 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Amadzudzula nyanja+ ndi kuiphwetsa ndipo amaumitsa mitsinje yonse.+

      Basana ndi Karimeli afota+ ndipo maluwa a mitengo ya ku Lebanoni nawonso afota.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena