Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mawu onsewa anthu adzawadziwa.+ Efuraimu ndi anthu okhala ku Samariya,+ adzawadziwa mawuwo chifukwa cha kudzikweza kwawo ndiponso chifukwa cha mwano wa mumtima mwawo. Pakuti iwo anena kuti:+

  • Hoseya 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Nthawi zonse ndikafuna kuchiritsa Isiraeli,+ zolakwa za Efuraimu ndi zoipa za Samariya+ zimaonekera.+ Iwo amachita zachinyengo+ ndipo anthu akuba amalowa m’nyumba komanso gulu la achifwamba limasakaza zinthu panja.+

  • Amosi 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena