Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ Salimo 107:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo amayamba kufuulira Yehova m’masautso awo,+Ndipo iye amawatulutsa m’mavuto awo.+ Yesaya 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu Yehova, pa nthawi ya masautso iwo atembenukira kwa inu.+ Mutawalanga, akhuthulira mitima yawo kwa inu m’pemphero lonong’ona.+
16 Inu Yehova, pa nthawi ya masautso iwo atembenukira kwa inu.+ Mutawalanga, akhuthulira mitima yawo kwa inu m’pemphero lonong’ona.+