2 Mafumu 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pake, Azariya anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anamuika m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide. Kenako Yotamu mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.+ 2 Mafumu 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 M’chaka chachiwiri cha Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, Yotamu+ mwana wa Uziya+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu. 1 Mbiri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehoasi anabereka Amaziya,+ Amaziya anabereka Azariya,+ Azariya anabereka Yotamu,+ 2 Mbiri 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yotamu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Mayi ake dzina lawo linali Yerusa+ mwana wa Zadoki.
7 Pambuyo pake, Azariya anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anamuika m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide. Kenako Yotamu mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.+
32 M’chaka chachiwiri cha Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, Yotamu+ mwana wa Uziya+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu.
27 Yotamu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Mayi ake dzina lawo linali Yerusa+ mwana wa Zadoki.