Miyambo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova anandipanga monga chiyambi cha njira yake.+ Ine ndiye ntchito yoyambirira pa ntchito zake zimene anakwaniritsa kalekale kwambiri.+ Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ panali wina wotchedwa Mawu,+ ndipo Mawuyo anali ndi Mulungu,+ komanso Mawuyo anali mulungu.*+ Yohane 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Yesu anati: “Ndithudi ndikukuuzani, Abulahamu asanakhaleko, ine n’kuti ndilipo kale.”+ Akolose 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso, iye ali patsogolo pa zinthu zina zonse,+ ndipo zinthu zina zonse zinakhalapo kudzera mwa iye.+ Chivumbulutso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+
22 “Yehova anandipanga monga chiyambi cha njira yake.+ Ine ndiye ntchito yoyambirira pa ntchito zake zimene anakwaniritsa kalekale kwambiri.+
1 Pa chiyambi,+ panali wina wotchedwa Mawu,+ ndipo Mawuyo anali ndi Mulungu,+ komanso Mawuyo anali mulungu.*+
17 Ndiponso, iye ali patsogolo pa zinthu zina zonse,+ ndipo zinthu zina zonse zinakhalapo kudzera mwa iye.+
14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+