Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+ Zekariya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Monga mmene munakhalira temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a nyumba ya Yuda ndi a nyumba ya Isiraeli,+ ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo mukonzeke kugwira ntchito.’+
10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+
13 Monga mmene munakhalira temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a nyumba ya Yuda ndi a nyumba ya Isiraeli,+ ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo mukonzeke kugwira ntchito.’+