Yeremiya 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Maganizo anga kwa inu ndikuwadziwa bwino. Ndikuganizira+ zokupatsani mtendere osati masoka,+ kuti mukhale ndi chiyembekezo chabwino ndiponso tsogolo labwino,’+ watero Yehova. Yeremiya 32:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “Yehova wanena kuti, ‘Monga mmene ndabweretsera anthu awa masoka aakulu onsewa, momwemonso ndidzawabweretsera zabwino zonsezi zimene ndikunena kuti ndidzawabweretsera.+ Mika 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni udzamva ululu waukulu ngati mkazi amene akumva kupweteka kwambiri pobereka.+ Tsopano uchoka m’tauni ndipo ukakhala kumudzi.+ Ukafika mpaka ku Babulo+ koma kumeneko udzapulumutsidwa.+ Kumeneko Yehova adzakuwombola m’manja mwa adani ako.+
11 “‘Maganizo anga kwa inu ndikuwadziwa bwino. Ndikuganizira+ zokupatsani mtendere osati masoka,+ kuti mukhale ndi chiyembekezo chabwino ndiponso tsogolo labwino,’+ watero Yehova.
42 “Yehova wanena kuti, ‘Monga mmene ndabweretsera anthu awa masoka aakulu onsewa, momwemonso ndidzawabweretsera zabwino zonsezi zimene ndikunena kuti ndidzawabweretsera.+
10 Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni udzamva ululu waukulu ngati mkazi amene akumva kupweteka kwambiri pobereka.+ Tsopano uchoka m’tauni ndipo ukakhala kumudzi.+ Ukafika mpaka ku Babulo+ koma kumeneko udzapulumutsidwa.+ Kumeneko Yehova adzakuwombola m’manja mwa adani ako.+