2 Samueli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Patapita nthawi, mfumu ndi anthu ake anapita ku Yerusalemu kukamenyana ndi Ayebusi+ amene anali kukhala kumeneko. Ayebusiwo anayamba kuuza Davide kuti: “Sulowa mumzinda uno, pakuti upitikitsidwa ndi anthu akhungu ndi olumala.”+ Mumtima mwawo iwo anali kunena kuti: “Davide sangalowe mumzinda uno.” 1 Mafumu 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu onse otsala a Aamori,+ Ahiti,+ Aperezi,+ Ahivi,+ ndi Ayebusi,+ amene sanali ana a Isiraeli,+ 1 Mbiri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pambuyo pake Davide ndi Aisiraeli onse anapita ku Yerusalemu,+ kapena kuti ku Yebusi,+ dziko limene kunali kukhala Ayebusi.+ 1 Mbiri 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Davide ataona kuti Yehova wamuyankha pamalo opunthira mbewu a Orinani Myebusi, anapitiriza kuperekera nsembe pamalopo.+
6 Patapita nthawi, mfumu ndi anthu ake anapita ku Yerusalemu kukamenyana ndi Ayebusi+ amene anali kukhala kumeneko. Ayebusiwo anayamba kuuza Davide kuti: “Sulowa mumzinda uno, pakuti upitikitsidwa ndi anthu akhungu ndi olumala.”+ Mumtima mwawo iwo anali kunena kuti: “Davide sangalowe mumzinda uno.”
20 Anthu onse otsala a Aamori,+ Ahiti,+ Aperezi,+ Ahivi,+ ndi Ayebusi,+ amene sanali ana a Isiraeli,+
4 Pambuyo pake Davide ndi Aisiraeli onse anapita ku Yerusalemu,+ kapena kuti ku Yebusi,+ dziko limene kunali kukhala Ayebusi.+
28 Davide ataona kuti Yehova wamuyankha pamalo opunthira mbewu a Orinani Myebusi, anapitiriza kuperekera nsembe pamalopo.+