Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 22:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+

      Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+

  • Yesaya 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’masiku otsiriza,+ phiri la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri,+ ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu yonse idzakhamukira kumeneko.+

  • Zekariya 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’masiku amenewo, amuna 10 ochokera m’zilankhulo zonse za anthu a mitundu ina+ adzagwira+ chovala cha munthu amene ndi Myuda+ ndi kunena kuti: “Anthu inu tipita nanu limodzi,+ chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.”’”+

  • Mateyu 28:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse+ kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ m’dzina la Atate,+ ndi la Mwana,+ ndi la mzimu woyera,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena