Salimo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+ Zefaniya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo ndidzapatsa mitundu ya anthu chilankhulo choyera+ kuti onse aziitanira pa dzina la Yehova+ ndi kumutumikira mogwirizana.’*+ Mateyu 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse+ kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ m’dzina la Atate,+ ndi la Mwana,+ ndi la mzimu woyera,+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+
9 Pamenepo ndidzapatsa mitundu ya anthu chilankhulo choyera+ kuti onse aziitanira pa dzina la Yehova+ ndi kumutumikira mogwirizana.’*+
19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse+ kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ m’dzina la Atate,+ ndi la Mwana,+ ndi la mzimu woyera,+
4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+