Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mneneri Yesaya ananenera za iyeyu+ m’mawu awa: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani+ njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.’”

  • Maliko 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova* anthu inu, wongolani misewu yake,’”+

  • Yohane 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake wofuula m’chipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+

  • Yohane 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Inu nomwe ndinu mboni zanga pamawu amene ndinanena kuti, Ine sindine Khristu,+ koma, ndinatumizidwa monga kalambulabwalo wake.+

  • Machitidwe 13:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mpulumutsi+ ameneyu asanafike, Yohane+ anali atalalikiriratu poyera kwa anthu onse mu Isiraeli za ubatizo, monga chizindikiro cha kulapa.

  • Machitidwe 19:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena