Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 28:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse+ kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ m’dzina la Atate,+ ndi la Mwana,+ ndi la mzimu woyera,+

  • Maliko 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako anaitana ophunzira 12 aja, ndipo anayamba kuwatumiza awiriawiri,+ ndi kuwapatsa mphamvu pa mizimu yonyansa.+

  • Luka 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho anawatumiza kukalalikira ufumu wa Mulungu ndi kuchiritsa anthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena