Levitiko 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usavule mkazi wa m’bale wako,+ chifukwa kumeneko n’kuvula m’bale wako. Levitiko 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwamuna akakwatira mkazi wa m’bale wake, wachita chinthu chonyansa.+ Iye wavula m’bale wake. Mwamuna ndi mkaziyo ayenera kufa kuti asabereke ana. Mateyu 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anachita zimenezi chifukwa Yohane anali kumuuza kuti: “N’kosaloleka kutenga mkaziyu kuti akhale mkazi wanu.”+ Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+
21 Mwamuna akakwatira mkazi wa m’bale wake, wachita chinthu chonyansa.+ Iye wavula m’bale wake. Mwamuna ndi mkaziyo ayenera kufa kuti asabereke ana.
4 Anachita zimenezi chifukwa Yohane anali kumuuza kuti: “N’kosaloleka kutenga mkaziyu kuti akhale mkazi wanu.”+
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+