Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chimene chimalowa m’kamwa sichiipitsa munthu, koma chotuluka m’kamwa mwake n’chimene chimaipitsa munthu.”+

  • Machitidwe 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma Petulo anati: “Iyayi Ambuye, sindinadyepo choipitsidwa ndi chonyansa chilichonse chikhalire.”+

  • 1 Akorinto 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma chakudya sichingatikometse pamaso pa Mulungu.+ Ngati sitinadye chakudyacho, sikuti tamulakwira, ndiponso ngati tadya, sikuti tamukondweretsa mwapadera.+

  • 1 Timoteyo 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndikutero chifukwa chakuti chilichonse cholengedwa ndi Mulungu n’chabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati chalandiridwa moyamikira,+

  • Tito 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Zinthu zonse n’zoyera kwa anthu oyera.+ Koma kwa anthu oipitsidwa+ ndi opanda chikhulupiriro+ kulibe choyera, m’malomwake maganizo awo ndi chikumbumtima+ chawo n’zoipa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena