Salimo 130:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mumakhululukiradi,+Kuti anthu akuopeni.+ Yesaya 43:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ineyo ndi amene ndikufafaniza+ zolakwa zako,+ ndipo machimo ako sindidzawakumbukiranso.+