Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 61:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 61 Mzimu wa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, uli pa ine,+ pakuti Yehova wandidzoza+ kuti ndikanene uthenga wabwino kwa anthu ofatsa.+ Wandituma kuti ndikamange zilonda za anthu osweka mtima,+ ndikalengeze za ufulu kwa anthu ogwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+ ndiponso ndikatsegule maso a akaidi.+

  • Mateyu 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye atamva zimenezo, anayankha kuti: “Anthu abwinobwino safuna dokotala,+ koma odwala ndi amene amamufuna.

  • Luka 5:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Poyankha, Yesu anawauza kuti: “Anthu athanzi safuna dokotala,+ koma odwala ndi amene amamufuna.+

  • Luka 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti Mwana wa munthu anabwera kudzafunafuna ndi kupulumutsa anthu osochera.”+

  • 1 Timoteyo 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mawu akuti Khristu Yesu anabwera m’dziko kudzapulumutsa ochimwa,+ ndi mawu oona ndi oyenera kuwavomereza ndi mtima wonse.+ Mwa ochimwa amenewa, ine ndiye wochimwa kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena