Salimo 119:136 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 136 Misozi yatsika m’maso mwanga ngati mitsinje ya madzi,+Chifukwa chakuti iwo sanasunge chilamulo chanu.+ Yeremiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+ Luka 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu anacheukira amayiwo ndi kunena kuti: “Ana aakazi a Yerusalemu inu, lekani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+ Yohane 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yesu anagwetsa misozi.+
136 Misozi yatsika m’maso mwanga ngati mitsinje ya madzi,+Chifukwa chakuti iwo sanasunge chilamulo chanu.+
9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+
28 Yesu anacheukira amayiwo ndi kunena kuti: “Ana aakazi a Yerusalemu inu, lekani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+