Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aefeso 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Munthu asakupusitseni ndi mawu opanda pake,+ pakuti mkwiyo wa Mulungu udzafika pa ana a kusamvera, ochita zinthu zimene ndatchulazi.+

  • 2 Atesalonika 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Wina asakunyengeni pa nkhani imeneyi m’njira iliyonse. Pakuti tsikulo silidzayamba kufika mpatuko+ usanachitike, ndiponso asanaonekere+ munthu wosamvera malamulo,+ amene ndiye mwana wa chiwonongeko.+

  • 2 Timoteyo 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma anthu oipa ndi onyenga adzaipiraipirabe. Iwo azidzasocheretsa ena ndiponso azidzasocheretsedwa.+

  • 1 Yohane 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,+ koma muziyesa mawu ouziridwawo kuti muone ngati ali ochokeradi kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri onyenga ambiri alowa m’dziko.+

  • Chivumbulutso 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena