Mateyu 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Khalani maso+ ndipo pempherani+ kosalekeza kuti musalowe m’mayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+ Maliko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Amuna inu, khalani maso ndipo muzipemphera,+ kuti musalowe m’mayesero. Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+ Luka 22:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Iye anawauza kuti: “Mukugona chifukwa chiyani? Dzukani, pitirizani kupemphera kuti musalowe m’mayesero.”+
41 Khalani maso+ ndipo pempherani+ kosalekeza kuti musalowe m’mayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+
38 Amuna inu, khalani maso ndipo muzipemphera,+ kuti musalowe m’mayesero. Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+
46 Iye anawauza kuti: “Mukugona chifukwa chiyani? Dzukani, pitirizani kupemphera kuti musalowe m’mayesero.”+