Mateyu 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ufumu wakumwamba uli ngati mfumu imene inakonza phwando la ukwati+ wa mwana wake. 2 Akorinto 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikukuchitirani nsanje,+ ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati+ ndi mwamuna mmodzi,+ Khristu,+ ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera+ kwa iye. Chivumbulutso 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya. Timupatse ulemerero,+ chifukwa ukwati+ wa Mwanawankhosa wafika,+ ndipo mkazi wake wadzikongoletsa.+
2 Ndikukuchitirani nsanje,+ ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati+ ndi mwamuna mmodzi,+ Khristu,+ ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera+ kwa iye.
7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya. Timupatse ulemerero,+ chifukwa ukwati+ wa Mwanawankhosa wafika,+ ndipo mkazi wake wadzikongoletsa.+