-
Mateyu 7:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndiyeno kunagwa chimvula champhamvu ndipo madzi anasefukira. Kenako chimphepo chinafika n’kuwomba nyumbayo, koma sinagwe chifukwa chakuti inakhazikika pathanthwepo.
-