Yesaya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akhale ngati malo opatulika.+ Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli, iye akhale ngati mwala wopunthwitsa ndiponso ngati mwala wokhumudwitsa.+ Akhalenso ngati msampha ndi khwekhwe kwa anthu okhala mu Yerusalemu.+ Mateyu 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wodala amene sapeza chokhumudwitsa mwa ine.”+ Luka 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Komanso, Simiyoni anadalitsa makolowo, ndipo anauza Mariya, mayi a mwanayo kuti: “Tamverani! Uyu waikidwa kuti ambiri agwe,+ ndiponso kuti ambiri adzukenso mu Isiraeli,+ ndi kuti akhale chizindikiro chimene anthu adzachitsutse+ Yohane 6:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Pa chifukwa chimenechi ophunzira ake ambiri anamusiya ndi kubwerera ku zinthu zakumbuyo,+ ndipo sanayendenso naye.+
14 Iye akhale ngati malo opatulika.+ Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli, iye akhale ngati mwala wopunthwitsa ndiponso ngati mwala wokhumudwitsa.+ Akhalenso ngati msampha ndi khwekhwe kwa anthu okhala mu Yerusalemu.+
34 Komanso, Simiyoni anadalitsa makolowo, ndipo anauza Mariya, mayi a mwanayo kuti: “Tamverani! Uyu waikidwa kuti ambiri agwe,+ ndiponso kuti ambiri adzukenso mu Isiraeli,+ ndi kuti akhale chizindikiro chimene anthu adzachitsutse+
66 Pa chifukwa chimenechi ophunzira ake ambiri anamusiya ndi kubwerera ku zinthu zakumbuyo,+ ndipo sanayendenso naye.+