Mateyu 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 anthu okhala mu mdima+ anaona kuwala kwakukulu,+ ndipo anthu okhala m’dera la mthunzi wa imfa, kuwala+ kunawatulukira.”+ Yohane 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa. 1 Yohane 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komabe, ndikukulemberani lamulo latsopano limene Yesu analitsatira, limenenso inuyo mukulitsatira, chifukwa chakuti mdima+ ukupita ndipo kuwala kwenikweni+ kwayamba kale kuunika.
16 anthu okhala mu mdima+ anaona kuwala kwakukulu,+ ndipo anthu okhala m’dera la mthunzi wa imfa, kuwala+ kunawatulukira.”+
19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa.
8 Komabe, ndikukulemberani lamulo latsopano limene Yesu analitsatira, limenenso inuyo mukulitsatira, chifukwa chakuti mdima+ ukupita ndipo kuwala kwenikweni+ kwayamba kale kuunika.