Yohane 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwala+ kwenikweni kumene kumaunikira+ anthu osiyanasiyana+ kunali pafupi kubwera m’dziko. Yohane 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala+ kwa dziko. Wonditsatira ine sadzayenda mumdima,+ koma adzakhala nako kuwala kwa moyo.” Akolose 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 pakuti zinthu zimenezo ndi mthunzi+ wa zimene zinali kubwera, koma zenizeni+ zake zili mwa Khristu.+
12 Pamenepo Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala+ kwa dziko. Wonditsatira ine sadzayenda mumdima,+ koma adzakhala nako kuwala kwa moyo.”
17 pakuti zinthu zimenezo ndi mthunzi+ wa zimene zinali kubwera, koma zenizeni+ zake zili mwa Khristu.+