Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 51:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mundisambitse bwinobwino ndi kuchotsa cholakwa changa,+

      Ndiyeretseni ku tchimo langa.+

  • 1 Akorinto 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+

  • Aefeso 5:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 ndipo anauyeretsa+ pousambitsa m’madzi a mawu a Mulungu.+

  • Tito 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye sanatero chifukwa cha ntchito+ zolungama zimene tinachita+ ayi. Koma malinga ndi chifundo+ chake, anatipulumutsa mwa kutisambitsa+ ndipo chifukwa chakuti tinasambitsidwa choncho, tinafika ku moyo+ watsopano. Komanso, anatipulumutsa potisandutsa atsopano mwa mzimu woyera.+

  • Aheberi 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 tiyeni timufikire Mulungu ndi mitima yoona. Tichite zimenezi tilibe chikayikiro chilichonse komanso tili ndi chikhulupiriro, pakuti mitima yathu yayeretsedwa* kuti isakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa m’madzi oyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena