Danieli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndiyeno m’masomphenya ausikuwo, ndinaonanso wina wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera m’mitambo.+ Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri uja,+ ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Iye.+ Mateyu 26:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Yesu anamuyankha+ kuti: “Mwanena nokha.+ Ndipo ndikukuuzani anthu inu kuti, kuyambira tsopano+ mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera pamitambo yakumwamba.”+ Chivumbulutso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Akubwera ndi mitambo,+ ndipo diso lililonse lidzamuona,+ ngakhalenso anthu amene anamulasa.+ Ndipo mafuko onse a padziko lapansi adzadziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye.+ Ame.
13 “Ndiyeno m’masomphenya ausikuwo, ndinaonanso wina wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera m’mitambo.+ Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri uja,+ ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Iye.+
64 Yesu anamuyankha+ kuti: “Mwanena nokha.+ Ndipo ndikukuuzani anthu inu kuti, kuyambira tsopano+ mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera pamitambo yakumwamba.”+
7 Taonani! Akubwera ndi mitambo,+ ndipo diso lililonse lidzamuona,+ ngakhalenso anthu amene anamulasa.+ Ndipo mafuko onse a padziko lapansi adzadziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye.+ Ame.