Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 chifukwa mumtima mwake anali kunena kuti: “Ndikangogwira malaya ake akunja okhawo, ndichira ndithu.”+

  • Mateyu 14:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Anthu anali kum’pempha kuti angogwira chabe ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo onse amene anaugwira anachiriratu.

  • Maliko 6:56
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 56 Ndipo akangolowa m’midzi, kapena m’mizinda, kapena m’madera ozungulira alionse,+ anthu anali kukhazika odwala m’misika. Iwo anali kum’dandaulira kuti angogwira+ chabe ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake+ akunja. Ndipo anthu ambiri anaugwira ndi kuchira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena