Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano mayi wina amene anali ndi nthenda yotaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake n’kugwira ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake akunja,+

  • Maliko 5:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Atamva zambiri zokhudza Yesu, anakalowa m’khamu la anthulo ndi kumudzera kumbuyo kwake, kenako anagwira+ malaya ake akunja.

  • Luka 8:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Mayiyu anamudzera kumbuyo Yesu n’kugwira ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa malaya ake akunja.+ Nthawi yomweyo anasiya kutaya magazi.+

  • Machitidwe 19:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Moti anthu anali kutenga ngakhale mipango yopukutira thukuta ndi maepuloni amene akhudza thupi la Paulo n’kupita nazo kwa odwala,+ ndipo matenda awo anali kutheratu. Mizimu yoipa nayonso inali kutuluka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena