Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 28:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma ophunzira 11 aja anapita ku Galileya,+ kuphiri kumene Yesu anakonza kukakumana nawo.

  • Machitidwe 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiponso, mwa maumboni ambiri otsimikizika, iye anadzionetsa kwa atumwiwo kuti ali moyo pambuyo pa zovuta zimene anakumana nazo.+ Iwo anamuona masiku onse 40, ndipo anali kuwauza za ufumu wa Mulungu.+

  • Machitidwe 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+

  • 1 Akorinto 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno anaonekeranso kwa abale oposa 500 pa nthawi imodzi, ndipo ambiri a iwo akali ndi moyo mpaka lero,+ koma ena anagona mu imfa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena