Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ngakhale zili choncho, si onse amene amadziwa zimenezi.+ Koma ena, pokhala ozolowera mafano enaake mpaka panopo, akamadya chakudya choperekedwa kwa fano amachidya monga choperekedwadi kwa fano,+ ndipo popeza chikumbumtima chawo n’chofooka, chimaipitsidwa.+

  • Afilipi 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo ine ndikupitiriza kupemphera kuti chikondi chanu chipitirire kukula,+ limodzi ndi kudziwa zinthu molondola,+ komanso kuzindikira zinthu bwino kwambiri.+

  • 2 Petulo 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa chifukwa chimenechi, nthawi zonse ndizikukumbutsani+ zinthu zimenezi, ngakhale kuti mukuzidziwa kale ndipo ndinu olimba m’choonadi+ chimene munachilandira.+

  • 1 Yohane 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndikukulemberani izi, osati chifukwa chakuti simudziwa choonadi,+ koma chifukwa chakuti mukuchidziwa,+ ndiponso chifukwa chakuti palibe bodza lililonse limene limachokera m’choonadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena