Aroma 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ndikulankhula kwa inu ochokera m’mitundu ina. Malinga n’kuti ndine mtumwi+ weniweni wotumidwa kwa mitundu ina,+ ndimalemekeza+ utumiki wanga,+ Agalatiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo ataona kuti ndapatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mmene Petulo anapatsidwira ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa,+ Agalatiya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 (pajatu iye amene anapatsa Petulo mphamvu yokhala mtumwi kwa anthu odulidwa ndi amene anapatsanso ine mphamvu+ kuti ndikalalikire kwa anthu a mitundu ina)
13 Tsopano ndikulankhula kwa inu ochokera m’mitundu ina. Malinga n’kuti ndine mtumwi+ weniweni wotumidwa kwa mitundu ina,+ ndimalemekeza+ utumiki wanga,+
7 Koma iwo ataona kuti ndapatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mmene Petulo anapatsidwira ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa,+
8 (pajatu iye amene anapatsa Petulo mphamvu yokhala mtumwi kwa anthu odulidwa ndi amene anapatsanso ine mphamvu+ kuti ndikalalikire kwa anthu a mitundu ina)