Machitidwe 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira ponseponse.+ Chiwerengero cha ophunzira chinali kuwonjezeka kwambiri mu Yerusalemu.+ Ndipo ansembe ambirimbiri+ anakhala okhulupirira.+ Tito 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu.
7 Pamenepo mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira ponseponse.+ Chiwerengero cha ophunzira chinali kuwonjezeka kwambiri mu Yerusalemu.+ Ndipo ansembe ambirimbiri+ anakhala okhulupirira.+
3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu.