1 Akorinto 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero ngati chakudya chikukhumudwitsa+ m’bale wanga, sindidzadyanso nyama m’pang’ono pomwe, kuti ndisakhumudwitse m’bale wanga.+ 1 Akorinto 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 sichichita zosayenera,+ sichisamala zofuna zake zokha,+ sichikwiya.+ Sichisunga zifukwa.+ Aefeso 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndiponso kuti mudziwe chikondi cha Khristu+ chimene chimaposa kudziwa zinthu zonse, kuti mudzazidwe ndi makhalidwe onse+ amene Mulungu amapereka.
13 Chotero ngati chakudya chikukhumudwitsa+ m’bale wanga, sindidzadyanso nyama m’pang’ono pomwe, kuti ndisakhumudwitse m’bale wanga.+
19 ndiponso kuti mudziwe chikondi cha Khristu+ chimene chimaposa kudziwa zinthu zonse, kuti mudzazidwe ndi makhalidwe onse+ amene Mulungu amapereka.