Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Mose anapanga njoka yamkuwa+ ndi kuiika pamtengo wachizindikirowo.+ Ndipo zinachitikadi kuti munthu akalumidwa ndi njoka n’kuyang’ana+ njoka yamkuwayo, anali kukhalabe ndi moyo.+

  • Yohane 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiponso, monga mmene Mose anakwezera njoka m’mwamba+ m’chipululu, momwemonso Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa m’mwamba,+

  • Yohane 19:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Popeza linali Tsiku Lokonzekera,+ Ayudawo sanafune kuti mitembo ikhalebe+ pamitengo yozunzikirapo tsiku la Sabata, (pakuti Sabata la tsiku limeneli linali lalikulu,)+ choncho anapempha Pilato kuti opachikidwawo awathyole miyendo ndi kutsitsa mitemboyo.

  • Machitidwe 5:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Mulungu wa makolo athu anaukitsa+ Yesu, amene inu munamupha mwa kumupachika pamtengo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena