Machitidwe 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+ Aefeso 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 N’chifukwa chake ndikukupemphani kuti musabwerere m’mbuyo poona masautso+ angawa, amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, pakuti akutanthauza ulemerero kwa inu.
22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+
13 N’chifukwa chake ndikukupemphani kuti musabwerere m’mbuyo poona masautso+ angawa, amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, pakuti akutanthauza ulemerero kwa inu.