Aheberi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 tidzapulumuka bwanji+ ngati tanyalanyaza+ chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutso chimenechi,+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.+ Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+ Aheberi 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa chifukwa chimenecho, Yesu wakhala chikole cha pangano labwino koposa.+ Chivumbulutso 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+
3 tidzapulumuka bwanji+ ngati tanyalanyaza+ chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutso chimenechi,+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.+
3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+