Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 24:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mawu awanso akupita kwa anthu anzeru:+ Si bwino kukondera poweruza.+

  • Mateyu 22:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Choncho anamutumizira ophunzira awo, limodzi ndi achipani cha Herode,+ ndipo iwo anati: “Mphunzitsi, tikudziwa kuti inu mumanena zoona ndipo mumaphunzitsa njira ya Mulungu m’choonadi, ndiponso simusamala kuti uyu ndani, chifukwa simuyang’ana maonekedwe a anthu.+

  • 1 Timoteyo 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndikukulamula mwamphamvu, pamaso pa Mulungu ndi Khristu Yesu+ ndiponso angelo ochita kusankhidwa, kuti uzitsatira malangizo amenewa popanda kuweruziratu. Usachite kanthu ndi maganizo okondera.+

  • Yakobo 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma nzeru+ yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena