Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 20
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Satana adzamangidwa kwa zaka 1,000 (1-3)

      • Amene adzalamulire ndi Khristu kwa zaka 1,000 (4-6)

      • Satana adzamasulidwa, kenako adzawonongedwa (7-10)

      • Akufa adzaweruzidwa pamaso pa mpando wachifumu woyera (11-15)

Chivumbulutso 20:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, ptsa. 23-24

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 287

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, ptsa. 30-31

    3/1/1991, tsa. 31

Chivumbulutso 20:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 12:3
  • +Ge 3:1
  • +Yoh 8:44
  • +Zek 3:1; Chv 12:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, ptsa. 23-24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 287-288

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, ptsa. 30-31

    9/1/1989, tsa. 12

Chivumbulutso 20:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:11
  • +Chv 20:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 287-288

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, ptsa. 30-31

    9/1/1989, tsa. 12

    Kukambitsirana, ptsa. 356-357

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 182-183

Chivumbulutso 20:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:15-17
  • +Mt 19:28; Lu 22:28-30; 2Ti 2:12; Chv 1:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 288-290

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/1990, tsa. 31

    9/1/1989, ptsa. 11-12

Chivumbulutso 20:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:15
  • +1Ak 15:23, 52; Afi 3:10, 11; 1At 4:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 19

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 290

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/1998, ptsa. 22-23

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 182

    Kukambitsirana, tsa. 112

Chivumbulutso 20:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 14:13
  • +Chv 2:11; 20:14
  • +1Ak 15:54
  • +1Pe 2:9
  • +Chv 1:6; 5:9, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 290-291

    Nsanja ya Olonda,

    9/1/1989, ptsa. 11-12

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 172-173

Chivumbulutso 20:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 19

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291-292

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 183

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/1987, ptsa. 31-32

    Mtendere Weniweni, ptsa. 53-54

Chivumbulutso 20:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 19

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 33

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2017, tsa. 29

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2015, tsa. 30

    5/15/2006, ptsa. 6-7

    12/1/2002, tsa. 29

    10/15/2000, tsa. 19

    10/15/1988, tsa. 20

    1/1/1987, ptsa. 31-32

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291-292

    Lambirani Mulungu, ptsa. 189-191

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 183

    Mtendere Weniweni, ptsa. 53-54

    Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 183

Chivumbulutso 20:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Mf 1:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 33

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291, 292-293, 304

    Lambirani Mulungu, ptsa. 189-191

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2000, tsa. 19

    2/1/1998, tsa. 22

    Mtendere Weniweni, ptsa. 53-54

Chivumbulutso 20:10

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “iwo adzaikidwa mʼndende.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:1
  • +Chv 19:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 33

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2008, tsa. 7

    4/1/2008, ptsa. 22-23

    5/15/2006, ptsa. 6-7

    11/15/2004, ptsa. 30-31

    11/1/1997, ptsa. 6-7

    4/15/1993, ptsa. 7-8

    12/15/1988, ptsa. 4-5

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 293-295

    Lambirani Mulungu, ptsa. 189-191

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 88

    Kukambitsirana, ptsa. 147-148

    Mtendere Weniweni, ptsa. 53-54

    Galamukani!,

    10/8/1986, tsa. 20

Chivumbulutso 20:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:2, 3
  • +2Pe 3:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 213

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 296

    Nsanja ya Olonda,

    8/1/1991, tsa. 5

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 181

Chivumbulutso 20:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 32:33; Sl 69:28; Da 12:1
  • +Yoh 5:28, 29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, ptsa. 18-19, 26

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2016, ptsa. 29-30

    3/2016, tsa. 22

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, ptsa. 213-214

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2010, tsa. 11

    3/15/2009, tsa. 12

    2/15/2009, tsa. 5

    1/15/2008, tsa. 28

    5/1/2005, tsa. 19

    8/15/1998, tsa. 30

    7/1/1998, tsa. 22

    8/1/1991, tsa. 6

    9/1/1987, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 296-297, 298-300, 310

    Lambirani Mulungu, tsa. 87

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 181-183

    Kukambitsirana, tsa. 111

Chivumbulutso 20:13

Mawu a M'munsi

  • *

    Amenewa ndi manda a anthu onse. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:42

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2008, tsa. 9

    5/1/2005, tsa. 19

    6/1/2000, tsa. 6

    4/1/1999, ptsa. 18-19

    8/1/1991, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 297

    Lambirani Mulungu, tsa. 87

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 181-182

    Kukambitsirana, ptsa. 111, 113

Chivumbulutso 20:14

Mawu a M'munsi

  • *

    Amenewa ndi manda a anthu onse. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 25:8; 1Ak 15:26
  • +Mt 5:22; 18:9; Chv 21:8
  • +Chv 2:11; 20:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2148

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2006, tsa. 31

    4/1/1999, ptsa. 18-19

    8/1/1991, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 300

    Lambirani Mulungu, ptsa. 86-87

    Kukambitsirana, tsa. 113

    Galamukani!,

    10/8/1986, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 20:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:8
  • +Miy 10:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 5

    8/1/1991, tsa. 6

    9/1/1987, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 300

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 183

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 20:1Chv 9:1
Chiv. 20:2Chv 12:3
Chiv. 20:2Ge 3:1
Chiv. 20:2Yoh 8:44
Chiv. 20:2Zek 3:1; Chv 12:9
Chiv. 20:3Chv 9:11
Chiv. 20:3Chv 20:7
Chiv. 20:4Chv 13:15-17
Chiv. 20:4Mt 19:28; Lu 22:28-30; 2Ti 2:12; Chv 1:6
Chiv. 20:5Mac 24:15
Chiv. 20:51Ak 15:23, 52; Afi 3:10, 11; 1At 4:16
Chiv. 20:6Chv 14:13
Chiv. 20:6Chv 2:11; 20:14
Chiv. 20:61Ak 15:54
Chiv. 20:61Pe 2:9
Chiv. 20:6Chv 1:6; 5:9, 10
Chiv. 20:92Mf 1:10
Chiv. 20:10Chv 13:1
Chiv. 20:10Chv 19:20
Chiv. 20:11Chv 4:2, 3
Chiv. 20:112Pe 3:7
Chiv. 20:12Eks 32:33; Sl 69:28; Da 12:1
Chiv. 20:12Yoh 5:28, 29
Chiv. 20:13Mac 10:42
Chiv. 20:14Yes 25:8; 1Ak 15:26
Chiv. 20:14Mt 5:22; 18:9; Chv 21:8
Chiv. 20:14Chv 2:11; 20:6
Chiv. 20:15Chv 17:8
Chiv. 20:15Miy 10:7
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 20:1-15

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

20 Ndipo ndinaona mngelo akutsika kuchokera kumwamba ali ndi kiyi wa phompho+ ndi tcheni chachikulu mʼdzanja lake. 2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ nʼkumumanga kwa zaka 1,000. 3 Ndipo anamuponyera mʼphompho+ nʼkutseka pakhomo la phompholo kenako anaikapo chidindo kuti asasocheretsenso mitundu ya anthu mpaka zaka 1,000 zitatha. Pambuyo pake, adzamasulidwa kanthawi kochepa.+

4 Kenako ndinaona mipando yachifumu ndipo amene anakhala pamipandoyo anapatsidwa mphamvu zoweruza. Ndinaona miyoyo ya anthu amene anaphedwa chifukwa chochitira umboni za Yesu komanso chifukwa cholankhula za Mulungu. Inde, ndinaona miyoyo ya anthu amene sanalambire chilombo kapena chifaniziro chake ndipo sanalandire chizindikiro pazipumi zawo ndi padzanja lawo.+ Iwo anakhalanso ndi moyo ndipo analamulira monga mafumu limodzi ndi Khristu+ kwa zaka 1,000. 5 (Akufa enawo+ sanakhalenso ndi moyo mpaka zaka 1,000 zitatha.) Uku ndi kuuka koyamba kwa akufa.+ 6 Wosangalala komanso woyera ndi aliyense amene akuuka nawo pa kuuka koyamba.+ Imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro pa amenewa.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi ndi Khristu zaka 1,000.+

7 Ndiye zaka 1,000 zimenezi zikadzangotha, Satana adzamasulidwa mʼndende yake, 8 ndipo adzatuluka kukasocheretsa mitundu ya anthu kumakona onse 4 a dziko lapansi. Mitunduyo ndi Gogi komanso Magogi ndipo adzaisonkhanitsa pamodzi kuti amenye nkhondo. Iwo ndi ochuluka ngati mchenga wakunyanja. 9 Iwo adzafalikira padziko lonse lapansi ndipo adzazungulira msasa wa oyera komanso mzinda wokondedwa. Koma moto udzatsika kuchokera kumwamba nʼkuwapsereza.+ 10 Mdyerekezi, amene ankawasocheretsa, adzaponyedwa mʼnyanja yamoto ndi sulufule, mmene muli kale chilombo+ ndi mneneri wabodza uja.+ Ndipo iwo adzazunzidwa masana ndi usiku* mpaka kalekale.

11 Kenako ndinaona mpando wachifumu waukulu woyera komanso Mulungu atakhala pampandowo.+ Dziko lapansi ndi kumwamba zinathawa pamaso pake+ ndipo sizinapezekenso. 12 Ndiye ndinaona akufa, olemekezeka ndi onyozeka, ataimirira pamaso pa mpando wachifumuwo, ndipo mipukutu inatambasulidwa. Koma panali mpukutu wina umene unatambasulidwa, womwe ndi mpukutu wa moyo.+ Akufa anaweruzidwa potengera zimene zinalembedwa mʼmipukutuyo, mogwirizana ndi ntchito zawo.+ 13 Nyanja inapereka akufa amene anali mmenemo. Imfa komanso Manda* zinapereka akufa amene anali mmenemo. Aliyense payekha anaweruzidwa mogwirizana ndi ntchito zake.+ 14 Ndipo imfa ndi Manda* zinaponyedwa mʼnyanja yamoto.+ Nyanja yamoto+ imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+ 15 Komanso, aliyense amene dzina lake silinalembedwe mʼbuku la moyo+ anaponyedwa mʼnyanja yamoto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena