Zamkatimu
May 2008
Kodi Muyenera Kuopa Zam’tsogolo?
Anthu ambiri masiku ano amaopa zam’tsogolo chifukwa cha mavuto osiyanasiyana amene alipowa. Koma kodi zam’tsogolo ziyeneradi kutiopsa? Kodi tsogolo lathu kwenikweni lili m’manja mwa anthu olemera, andale, azipembedzo, ndi asayansi? Werengani nkhaniyi kuti muone yankho lolimbikitsa la mafunso amenewa.
3 N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Akuopa Zam’tsogolo?
4 Kodi Anthu Angabweretse Tsogolo Labwino?
7 Tsogolo Labwino mu Ulamuliro wa Mulungu
19 Kodi Mphatso Zachifundo Zingathetse Mavuto Athu Onse?
22 Nyimbo Ndi Mphatso ya Mulungu Yotitsitsimula
24 Kanyanja Kokongola Kwambiri
32 “Dalitsidwani ndi Mfumu Yotsogoleredwa ndi Mzimu wa Yehova”
Mtundu wa Anthu Umene Unatenga Malo ku Asia 12
Werengani nkhaniyi kuti mumve za mtundu wa anthu okonda kuyenda pa mahatchi, umene pa zaka 25 zokha unagonjetsa madera ambiri kuposa madera onse amene Aroma anagonjetsa pa zaka 400.
Chaka chilichonse, achinyamata ambiri amadzipha ndipo palinso ochuluka amene amayesa kutero. Werengani nkhaniyi kuti muone mmene munthu angathetsere maganizo amene amachititsa kufuna kudzipha.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Horsemen: Bildarchiv Preussischer Kulturbesitz/Art Resource, NY