Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w15 12/15 tsamba 32
  • Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2015

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2015
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
w15 12/15 tsamba 32

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2015

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

BAIBULO

  • Baibulo la Bedell (Ireland), 9/1

  • Baibulo la Dziko Latsopano Lokonzedwanso Lomwe Linatuluka mu 2013, 12/15

  • Kodi Mungakonde Kuliphunzira? 4/1

  • Kodi Sayansi Ingalilowe M’malo? 6/1

  • Ku Japan Analandira Mphatso (Mateyu), 2/15

  • Maulosi, 9/1

  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuliwerenga? 2/1

  • N’zotheka Kumvetsa Zimene Limanena, 12/1

  • Zinthu Zamtengo Wapatali Zimene Anapeza Pamulu wa Zinyalala, 4/1

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

  • Baibulo Linandithandiza Kupeza Mayankho (M. Gündel), 1/1

  • Mafunso Atatu Omwe Anasintha Moyo Wanga (D. Eldred), 4/1

  • Mayankho a Mafunso Anga (E. Loedi), 2/1

  • Moyo Wanga Unkangoipiraipirabe (S. McDowell), 7/1

  • Ndinaphunzira Kuti Yehova Ndi Wachifundo (N. Pelletier), 5/1

  • Ndinkaona Ngati Zinthu Zikundiyendera (P. Pyzara), 11/1

  • Panopa Ndimaona Kuti Ndingathe Kuthandiza Ena (J. Corio), 10/1

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

  • Abale ndi alongo amene amavutika akamva fungo la perefyumu, 2/15

  • Kodi Gogi wa kudziko la Magogi ndi ndani? 5/15

  • Kodi mlongo azivala chinachake kumutu pochititsa phunziro ndi m’bale amene ndi wofalitsa? 2/15

  • Kodi mzinda wakale wa Yeriko unagonjetsedwa m’kanthawi kochepa? 11/15

  • N’chifukwa chiyani safotokozanso kuti zinthu zosiyanasiyana zimaphiphiritsira zinazake? 3/15

  • Pontiyo Pilato analikodi? 2/15

MBIRI YA MOYO WATHU

  • Chikondi Changa cha Poyamba Chandithandiza Kupirira (A. Morris III), 5/15

  • Chuma Chomwe Chakhala ku Banja Lathu kwa Mibadwo 7 (K. Williams), 6/1

  • Jairo Amagwiritsa Ntchito Maso Ake Kutumikira Mulungu, 3/1

  • Madalitso a Yehova Andilemeretsa (M. Jaracz), 9/15

  • Ndadalitsidwa “M’nthawi Yabwino ndi M’nthawi Yovuta” (T. R. Nsomba), 4/15

  • Ndili pa Mtendere ndi Mulungu Komanso Amayi Anga (M. Kumagai), 12/15

  • Ndinapeza Chinthu Chamtengo Wapatali Kuposa Kukhala Wotchuka (M. H. Godenzi), 9/1

  • Tinapeza Ntchito Yabwino Kwambiri (D. ndi G. Cartwright), 3/15

  • Yehova Wandichitira Zazikulu (F. Alarcón), 8/1

  • “Zilumba Zambiri Zisangalale” (G. Jackson), 8/15

  • Zimene Anasankha Ali Mnyamata (N. Dubovinsky), 10/15

MBONI ZA YEHOVA

  • Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku New York, 1/15

  • Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Russia, 7/15

  • Kodi a Mboni za Yehova Mumawadziwa Bwinobwino? 9/1

  • Kuchotsa Anthu Osalapa Kumathandiza, 4/15

  • Kuyandikira kwa Mulungu Ndi Kwabwino (S. Maiga), 10/15

  • “Musalole Kuti Chilichonse Chikulepheretseni” (akopotala a ku France), 11/15

  • “Ngati Kingsley Akukwanitsa, Kuli Bwanji Ine?” 6/15

  • “Nyengo Yofunika Kwambiri” (Chikumbutso), 2/15

  • Tizilemekeza Kwambiri Abale Ngati Amenewa (abale amene amathandiza Bungwe Lolamulira), 10/15

  • Tiziyamikira Zimene Yehova Amatipatsa (zopereka), 11/15

  • “Yehova Anakubweretsani ku France Kuti Muphunzire Baibulo” (Anthu a ku Poland amene anapita ku France), 8/15

  • Zinthu Zinkayenda Bwino Chifukwa cha Chikondi, 5/15

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

  • Amuna Angatani Kuti Akazi Awo Azisangalala? 1/1

  • Kodi Kupemphera N’kothandizadi? 10/1

  • Kodi Mungadandaule Ngati Anthu Saona Ntchito Yanu? 7/15

  • Kodi N’zothekadi Kukwatira “mwa Ambuye”? 3/15

  • Kutumikira Yehova ‘M’masiku Oipa,’ 7/15

  • “Mukufunika Kupirira,” 6/15

  • ‘Munthu Wosadziwa Zinthu Amakhulupirira Mawu Alionse,’ 10/15

  • Muzikhululuka ndi Mtima Wonse, 10/1

  • Muzisangalala ndi Ntchito Yanu, 2/1

  • Tizikondabe Kulalikira, 2/15

NKHANI ZOPHUNZIRA

  • Ankaona Malonjezo Ali Patali, 5/15

  • Baibulo Lomveka Bwino Kwambiri, 12/15

  • “Chipulumutso Chanu Chikuyandikira,” 7/15

  • Khalani Maso, Satana Akufuna Kukumezani, 5/15

  • Khalani ndi Chikhulupiriro Cholimba, 9/15

  • Khalani Odzichepetsa Ndiponso Achifundo Ngati Yesu, 2/15

  • Khalani Olimba Mtima Ndiponso Ozindikira Ngati Yesu, 2/15

  • Khristu Ndiye Mphamvu ya Mulungu, 6/15

  • Kodi Chikumbumtima Chanu Chimakuthandizani Kusankha Zochita Mwanzeru? 9/15

  • Kodi ‘Mudzakhalabe Maso’? 3/15

  • Kodi Mukuyesetsa Kukhala Ngati Khristu? 9/15

  • Kodi ‘Mumakonda Anzanu Ngati Mmene Mumadzikondera Nokha’? 11/15

  • Kodi Mumaona Dzanja la Mulungu Likukuthandizani? 10/15

  • Kodi Mumaphunzitsa Ena Kuti Akhalenso Akulu? 4/15

  • Kodi N’zotheka Kukondana Mpaka Kalekale? 1/15

  • Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Fanizo la Matalente? 3/15

  • Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Yehova? 9/15

  • Kodi Yehova Amasonyeza Bwanji Kuti Amatikonda? 9/15

  • Kodi Yehova Ndi Mnzanu Weniweni? 4/15

  • Limbitsani Banja Lanu Kuti Likhale Losangalala, 1/15

  • Lolani Kuti Yehova Alimbitse Ndiponso Kuteteza Banja Lanu, 1/15

  • “Munavomereza Kuti Zimenezi Zichitike,” 3/15

  • Muzigwiritsa Ntchito Bwino Lilime Lanu, 12/15

  • Muzikhulupirira Yehova Nthawi Zonse, 4/15

  • Muziphunzitsa Ana Anu Aang’ono Kuti Azitumikira Yehova, 11/15

  • Muziphunzitsa Ana Anu Achinyamata Kuti Azitumikira Yehova, 11/15

  • N’chifukwa Chiyani Timachita Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu? 1/15

  • N’zotheka Kugonjetsa Satana, 5/15

  • N’zotheka Kukhalabe Oyera, 6/15

  • Pitirizani Kukhala Okhulupirika kwa Mulungu, 7/15

  • Tisalole Chilichonse Kutisokoneza Potumikira Yehova, 10/15

  • “Tiwonjezereni Chikhulupiriro,” 10/15

  • Tizichita Zinthu Mogwirizana ndi Pemphero la Ambuye, 6/15

  • Tiziganizira Kwambiri Chikondi cha Yehova, 8/15

  • Tiziganizira Kwambiri za Yehova, 10/15

  • Tizikonzekera Moyo wa M’dziko Latsopano, 8/15

  • Tizilemekeza Malo Athu Olambirira Yehova, 7/15

  • Tizisankha Mwanzeru Anthu Ocheza Nawo M’masiku Otsiriza Ano, 8/15

  • Tizithandiza Abale a Khristu Mokhulupirika, 3/15

  • Tizithandiza Kukongoletsa Gulu la Yehova, 7/15

  • Tiziyembekezerabe, 8/15

  • Tsanzirani Amene Wakulonjezani Moyo Wosatha, 5/15

  • Yamikani Yehova Ndipo Adzakudalitsani, 1/15

  • Yehova Adzakuthandizani Pamene Mukudwala, 12/15

  • Yehova Akutsogolera Ntchito Yolalikira Padziko Lonse, 2/15

  • Yehova Amalankhula Nafe, 12/15

  • Yehova Ndi Mulungu Wachikondi, 11/15

  • Yesu Amakonda Anthu, 6/15

  • Zimene Mungachite Pophunzitsa Ena Kuti Akhale Akulu, 4/15

  • Zimene Zachitika M’zaka 100 Zimene Ufumu Wakhala Ukulamulira, 11/15

  • Zinthu Zimene Zinathandiza Kuti Anthu Aphunzire za Yehova, 2/15

NKHANI ZOSIYANASIYANA

  • Abusa Ankalekanitsa Nkhosa ndi Mbuzi, 1/1

  • Opita ku Zikondwerero ku Yerusalemu Ankagona Kuti? 12/1

  • Boma Limodzi Lolamulira Dziko Lonse, 2/1

  • Boma Lopanda Chinyengo, 1/1

  • “Ine Ndinauka Monga Mayi mu Isiraeli” (Debora), 8/1

  • Kachisi wa Herode, 10/1

  • Kapitawo wa Asilikali Achiroma, 4/1

  • Kodi Akhristu Ayenera Kukondwerera Isitala? 3/1

  • Kodi Akufa Adzakhalanso ndi Moyo? 11/1

  • Kodi Anthu Adzakhala ndi Moyo Wotani M’tsogolo? 4/1

  • Kodi Anthu Adzasiya Kuchita Zachinyengo? 12/1

  • Kodi Anthu Akale Ankagwiritsa Ntchito Bwanji Mphero? 7/1

  • Kodi Anthu Amene Anamwalira Adzakhalanso ndi Moyo? 8/1

  • Kodi Ayuda Omwe Anabwera pa Pentekosite mu 33 C.E. Anachokeradi ‘mu Mtundu Uliwonse’? 12/1

  • Kodi Bambo a Timoteyo Anali Wochokera ku Girisi? 11/1

  • “Kodi Ine Ndatenga Malo a Mulungu?” (Yosefe), 5/1

  • Kodi Kale Abusa Ankawalipira Bwanji? 3/1

  • Kodi ku Isiraeli Kunali Mitengo Yambiri? 7/15

  • Kodi Mapeto Ali Pafupidi? 5/1

  • Kodi Mulungu Adzathetsa Bwanji Kudzikonda? 4/1

  • Kodi Mulungu Anatilengeranji? 8/1

  • Kodi Mungatani Kuti Mukhale Makolo Abwino? 6/1

  • Kodi Pali Winawake Amene Analenga Zonse? 1/1

  • Kodi Petulo Anali Papa Woyamba? 12/1

  • Kodi Tikuphunzira Chiyani kwa Jowana? 8/15

  • Kodi Tinalengedwa Kuti Tizingokhalako kwa Nthawi Yochepa? 8/1

  • Kuda Nkhawa, 7/1

  • ‘Kukhala Pachifuwa,’ 7/1

  • Magalasi Odziyang’anira Akale, 4/1

  • Mawu Achigiriki Akuti Eu nou’khos, 1/1

  • Mikango Inasiya Kupezeka M’madera Otchulidwa M’Baibulo, 5/1

  • Miyambo ya pa Khirisimasi, 12/1

  • Mphatso Zoyenera Kupatsa Mfumu (zinthu zonunkhira), 3/1

  • Mtengo Ukadulidwa Umaphukanso? 4/15

  • ‘Mulungu Ndiye Amamasulira Maloto?’ (Yosefe), 2/1

  • Mungatani Kuti Ana Anu Akule Bwino? 6/1

  • Mungatani Kuti Muzisangalalabe Ngakhale Mutakalamba? 6/1

  • “Mwana Wanga Wokondedwa ndi Wokhulupirika mwa Ambuye” (Timoteyo), 11/1

  • N’chifukwa Chiyani Anthu a ku Melita Ankaganiza Kuti Paulo Ndi Chigawenga? 10/1

  • N’chifukwa Chiyani Yosefe Anayamba Wameta Asanakaonane ndi Farao? 11/1

  • N’chiyani Chimachititsa Kuti Anthu Azichita Zoipa? 7/1

  • Nzika ya Roma, 3/1

  • Okana Khristu, 6/1

  • Opita ku Zikondwerero ku Yerusalemu Ankagona Kuti? 12/1

  • Tsiku la Chiweruzo, 5/1

  • Umphawi Udzathadi Padzikoli, 10/1

  • Zimene Ofukula Zinthu Zakale Anapeza Zimagwirizana ndi Baibulo? 5/1

YEHOVA

  • Kodi Amagwirizana ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo? 11/1

  • Kodi Mumamuimba Mlandu? 9/1

  • Kodi Ndi Wosamvetsetseka? 10/1

  • Kodi N’zotheka Kumudziwadi? 12/1

  • Kodi Tingamusangalatsedi? 7/1

YESU KHRISTU

  • Anatipulumutsa ku Uchimo ndi Imfa, 3/1

  • Kodi Tizipemphera kwa Iye? 1/1

  • Kukumbukira Imfa Yake, 3/1

  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukumbukira Imfa Yake? 4/1

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena