Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 10/13 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa October 14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa October 14
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 14
Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
km 10/13 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa October 14

MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 14

Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 2 ndime 7-13 ndi bokosi patsamba 20 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Afilipi 1-4 mpaka Akolose 1-4 (Mph. 10)

Na. 1: Afilipi 3:17 mpaka 4:1-9 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Kodi N’zoyenera Kusiya Chipembedzo Chimene Munabadwira?—rs tsa. 85 ndime 2-4 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Pemphero Lingatithandize Bwanji Kuthana Ndi Mayesero?—Luka 11:9-13; Yak. 1:5 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 68

Mph. 15: Mgwirizano Wathu wa Padziko Lonse Umalemekezetsa Yehova. Nkhani yochokera m’buku la Gulu, kuyambira patsamba 165 ndime 2 mpaka pakamutu ka patsamba 168. Pemphani omvera kuti anene nkhani zolembedwa m’mabuku athu zosonyeza kuti mgwirizano komanso chikondi chimene a Mboni ena anasonyeza zinathandiza kuti anthu ena alemekeze Yehova.

Mph. 15: “M’mwezi wa November Tidzagwira Ntchito Yogawira Kapepala ka Uthenga wa Ufumu Na. 38.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho. Gawirani munthu aliyense kapepala ka Uthenga wa Ufumu Na. 38. Funsani woyang’anira utumiki za dongosolo limene mpingo wanu wakonza zokhudza kulowa mu utumiki. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza zimene tingachite pogawira kapepalaka pogwiritsa ntchito chitsanzo cha ulaliki chimene chili patsamba 4.

Nyimbo Na. 53 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena