Zimene Zili M’magaziniyi
M’MAGAZINIYI MULI
Nkhani Yophunzira 48: February 2-8, 2026
2 Buku la Yobu Lingatithandize Tikamakumana Ndi Mavuto
Nkhani Yophunzira 49: February 9-15, 2026
8 Buku la Yobu Lingatithandize Tikamapereka Malangizo
Nkhani Yophunzira 50: February 16-22, 2026
14 Muzitsanzira Yehova pa Nkhani Yodzichepetsa
Nkhani Yophunzira 51: February 23, 2026–March 1, 2026
20 Zimene Mungachite Kuti Tsiku la Ukwati Wanu Lidzakhale Lolemekeza Yehova