December Nsanja ya Olonda Yophunzira Zimene Zili M’magaziniyi NKHANI YOPHUNZIRA 48 Buku la Yobu Lingakuthandizeni Mukamakumana ndi Mavuto NKHANI YOPHUNZIRA 49 Buku la Yobu Lingatithandize Tikamapereka Malangizo NKHANI YOPHUNZIRA 50 Muzitsanzira Yehova pa Nkhani Yodzichepetsa NKHANI YOPHUNZIRA 51 Zimene Mungachite Kuti Tsiku la Ukwati Wanu Lidzakhale Lolemekeza Yehova Achikulire—Ndinu Ofunika Kwambiri Mumpingo Kodi Mukukumbukira? MFUNDO ZOTHANDIZA POPHUNZIRA Zimene Mungachite Kuti Muzikhulupirira Kwambiri Kuti Yehova Ali Ndi Mphamvu Zotha Kupulumutsa