January Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya January 2020 Zimene Tinganene January 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 1-2 Yehova Analenga Zamoyo Padziko Lapansi MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira? January 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 3-5 Mavuto Omwe Anabwera Chifukwa cha Bodza Loyamba MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Tingayambe Bwanji Kukambirana ndi Anthu Pogwiritsa Ntchito Timapepala? January 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 6-8 “Anachitadi Momwemo” January 27–February 2 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 9-11 “Dziko Lonse Lapansi Linali ndi Chilankhulo Chimodzi” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzigwira Ntchito Yanu Mwaluso