Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • rsg19
  • Dziko la Satana

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Dziko la Satana
  • Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019
  • Timitu
  • Maboma a Anthu
  • Kuphwanya Malamulo Ndiponso Zachiwawa
  • Nkhondo
  • Nkhani Zokhudza Chikhalidwe cha Anthu
  • Zamalonda
  • Zokhudza Zachilengedwe
  • Mzimu wa Dziko
  • Zizolowezi Zoipa
  • Njira Zoperekera Mauthenga
  • Aramagedo
Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019
rsg19

Dziko la Satana

Onaninso pamutu wakuti Yehova Mulungu ➤ Chifukwa Chake Mulungu Walola Zinthu Zoipa Komanso Kuti Anthu Azivutika

❐ Nsanja ya Olonda, 10/1/2012

Ziphuphu​—Zili Ponseponse

N’Chifukwa Chiyani Anthu Akupitirizabe Kuchita Ziphuphu?

Kodi N’zotheka Kuchita Zinthu Mwachilungamo M’Dziko Laziphuphuli?

Ziphuphu Zidzatha

❐ Galamukani!, 7/2012

Kodi Inuyo Mungakonde Kusintha Zinthu Ziti?

Kodi N’chiyani Chikuyenera Kusintha?

Kodi Posachedwapa Chisinthe N’chiyani?

N’chifukwa Chiyani Anthu Amachita Zoipa? Nsanja ya Olonda, 9/1/2010

Maboma a Anthu

Onaninso pamutu wakuti Mboni za Yehova ➤ Zokhudza Kuchita Zinthu ndi Akuluakulu a Boma

Mafunso Ochokera kwa Owerenga: Kodi Mkhristu angadziwe bwanji ngati n’zoyenera kupereka ndalama kwa ogwira ntchito m’boma? Nsanja ya Olonda (Yophunzira), 5/2016

❐ Nsanja ya Olonda, 1/1/2015

M’mayiko Ambiri Mukuchitika Zachinyengo

Ufumu wa Mulungu Ndi Boma Lopanda Chinyengo

Ulamuliro wa Satana Utha Posachedwa Nsanja ya Olonda, 1/15/2010

Kodi Anthu Angabweretse Tsogolo Labwino? Galamukani!, 5/2008

❐ Nsanja ya Olonda, 8/1/2004

Kufunafuna Boma Labwino

Boma la Ufumu wa Mulungu Likuchita Zooneka

❐ Nsanja ya Olonda, 4/1/2004

666​—Si Nambala Yongodabwitsa Chabe

Kudziwa Chilombo ndi Chizindikiro Chake

Kodi Anthu Ofuna Kusintha Zinthu Angakwanitse Kutero? Galamukani!, 4/8/2004

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Zokambirana za Mayiko Zidzabweretsa Mtendere Padziko Lonse? Galamukani!, 1/8/2004

Kodi Mphamvu Zoipa Zapambana? (Kamutu: Kodi Anthu Angadzilamulire Okha Bwinobwino?) Nsanja ya Olonda, 1/15/2003

❐ Nsanja ya Olonda, 3/15/2002

Vuto la Utsogoleri Wabwino Lili Padziko Lonse

Kodi Utsogoleri Wabwino Tingaupeze Kuti?

Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse

13 Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse Oloseredwa ndi Danieli Kabuku Kothandiza Kuphunzira

❐ Nsanja ya Olonda, 6/15/2012

Yehova Ndi “Woulula Zinsinsi”

Yehova Waulula “Zimene Ziyenera Kuchitika Posachedwapa”

Yehova Anaulula Mafumu 8 (Tchati) Nsanja ya Olonda, 6/15/2012

Mafunso Ochokera kwa Owerenga: Kodi ulamuliro wa 7 wotchulidwa mu ulosi wa m’Baibulo unakhala liti ulamuliro wamphamvu padziko lonse? Nsanja ya Olonda, 6/15/2012

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira​—Gawo 1: Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ufumu wa Iguputo Galamukani!, 11/2010

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira​—Gawo 2: Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ufumu wa Asuri Galamukani!, 12/2010

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira​—Gawo 3: Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ufumu wa Babulo Galamukani!, 1/2011

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira​—Gawo 4: Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ufumu wa Mediya ndi Perisiya Galamukani!, 2/2011

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira​—Gawo 5: Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ufumu wa Girisi Galamukani!, 3/2011

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira​—Gawo 6: Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ufumu wa Roma Galamukani!, 4/2011

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira​—Gawo 7: Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ufumu Womaliza Kulamulira Dziko Lonse Galamukani!, 5/2011

United Nations (UN)

Yehova Waulula “Zimene Ziyenera Kuchitika Posachedwapa” Nsanja ya Olonda, 6/15/2012 ¶13-17

Kuphwanya Malamulo Ndiponso Zachiwawa

Kodi Zachiwawa Zidzatha Padzikoli? Nsanja ya Olonda (Yogawira), Na. 4 2016

Zimene Baibulo Limanena: Chiwawa Galamukani!, 5/2015

Nzeru Zomwe Zimateteza Galamukani!, 2/2015

Chenjerani ndi Mbava Komanso Anthu Ogwiririra Galamukani!, 5/2013

❐ Galamukani!, 8/2012

Aliyense Amakhudzidwa ndi Zachiwawa

Zachiwawa Zili Paliponse

N’chifukwa Chiyani Anthu Amachita Zachiwawa?

N’zotheka Kuyamba Kuchita Zinthu Mwamtendere

Ndinkakonda Kuchita Zachiwawa

Chenjerani ndi Zigawenga za pa Intaneti Galamukani!, 5/2012

Kodi Zachiwawa Zingathetsedwe? Galamukani!, 2/2008

Kuchitira Nkhanza Akazi Ndi Vuto la Padziko Lonse Galamukani!, 1/2008

Dzitetezeni Kuti Asakubereni Galimoto! Galamukani!, 10/2006

Kodi Ziwawazi Zachulukiranji Chonchi? Galamukani!, 7/8/2003

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Mulungu Amachiona Bwanji Chiwawa? Galamukani!, 8/8/2002

Kutetezedwa ndi Apolisi N’kolimbitsa Mtima Komanso N’kokayikitsa Galamukani!, 7/8/2002

Kodi Njira Yothetsera Vutolo Ndiyo Ikulikulitsanso? Galamukani!, 5/8/2001

❐ Galamukani!, 7/8/2000

Kodi Moyo Ukutsikiratsikira Mtengo?

Kodi “Chikhalidwe cha Imfa” Chimalimbikitsidwa Motani?

Kuthandiza Achinyamata Kuthawa “Chikhalidwe cha Imfa”

Kodi Anthu Achiwawa Mumawaona Monga Momwe Mulungu Amawaonera? Nsanja ya Olonda, 4/15/2000

Kuchitira Nkhanza Ana

Mmene Mungatetezere Ana Anu Galamukani!, 10/2007

❐ Galamukani!, 2/8/2003

“Nkhanza Zosaneneka”

N’chifukwa Chiyani Vutoli Likukula?

Vutoli Litha Posachedwapa!

Mmene Yesu Anatetezedwera Mphunzitsi Waluso, mutu 32

Mungachite Moyenera Ngakhale Sanakulereni Bwino Nsanja ya Olonda, 4/15/2001

Phunzitsani Mwana Wanu Kuyambira Paukhanda Wake (Kamutu: Tetezerani Mwana Wanu ku Ngozi) Chinsinsi cha Banja, mutu 5

Kugwiririra

Kodi Ndiyenera Kudziwa Chiyani Zokhudza Anthu Ogwiririra? Mayankho a Mafunso 10, funso 8

Mafunso Ochokera kwa Owerenga: N’chifukwa chiyani munthu ayenera kufuula ngati wina akufuna kumugwirira? Nsanja ya Olonda, 2/1/2003

Nkhanza Zokhudza Kugonana

Kodi Ndingatani Anzanga Akamandivutitsa Kusukulu? (Kamutu: Kodi Mungatani Ena Akamakuchitirani Zachipongwe?) Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 14

N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Amakhala Mwamantha? (Kamutu: Kuchitidwa Zachipongwe Kumaopsa Kwambiri) Galamukani!, 8/8/2005

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndingachitenji Ndikamavutitsidwa ndi Amuna Kapena Akazi? Galamukani!, 9/8/2000

Kuba

Kodi Masomphenya a Zekariya Akukukhudzani Bwanji? Nsanja ya Olonda (Yophunzira), 10/2017

❐ Galamukani!, 7/8/2005

Kodi Kuba M’masitolo Ndi Nkhani Yaikulu Bwanji?

N’chifukwa Chiyani Anthu Amaba M’masitolo?

Kodi Ndani Amavutika Chifukwa cha Kuba M’masitolo?

Mmene Munthu Angasiyire Kuba M’masitolo

Mmene Mungadzitetezere kwa Anthu Oba Mwachinyengo Galamukani!, 8/8/2004

Kuba Mwachinyengo ndi Vuto Lapadziko Lonse Galamukani!, 8/8/2004

Usakhale Wakuba! Mphunzitsi Waluso, mutu 24

Uchigawenga

“Mulungu Akutithandiza Kuti Tiiwale Zakale” Galamukani!, 5/2015

❐ Galamukani!, 6/2011

“Ndinangopitira Kukatenga Makalata Basi”

N’chifukwa Chiyani Anthu Amachita Zauchigawenga?

Kodi Uchigawenga Udzatha Padzikoli?

❐ Galamukani!, 6/2006

Ana Akuvutika ndi Uchigawenga

Mbiri Yodzaza ndi Kukhetsa Magazi

“Musaope, Kapena Kutenga Nkhawa” (Kamutu: Kusalowerera M’zinthu za M’dziko kwa Akhristu N’kosiyana ndi Uchigawenga) Nsanja ya Olonda, 6/1/2003

Tsiku Limene Nyumba Zosanja Ziwiri Zinagwa Galamukani!, 1/8/2002

Kulimbana ndi Vuto la Uchigawenga Galamukani!, 6/8/2001

Kuphedwa kwa Anthu Ambiri

“Ambuye, N’chifukwa Chiyani Simunachitepo Kanthu?” Nsanja ya Olonda, 5/15/2007

Kukumbukira Mboni za Yehova Zimene Zinaphedwa Nsanja ya Olonda, 1/15/2003

Olengeza Ufumu Akusimba: Anthu Amakono Ofera Chikhulupiriro Akuchitira Umboni ku Sweden Nsanja ya Olonda, 2/1/2002

Nkhondo

Zimene Baibulo Limanena: Nkhondo Galamukani!, Na. 5 2017

❐ Nsanja ya Olonda, 11/1/2015

Kodi Mulungu Amagwirizana ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo?

Kodi Mulungu Ankagwirizana ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo M’nthawi ya Aisiraeli?

Kodi Mulungu Ankagwirizana ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo M’nthawi ya Atumwi?

Kodi Mulungu Amagwirizana ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo Masiku Ano?

Nkhondo ya ku Ain Jalut Inasintha Zinthu Galamukani!, 3/2012

Zimene Baibulo Limanena: N’chifukwa Chiyani Mulungu Salola Akhristu Kumenya Nkhondo? Galamukani!, 8/2011

N’chifukwa Chiyani Mulungu Anawononga Akanani? Nsanja ya Olonda, 1/1/2010

Kodi Akhristu Ayenera Kumenya Nawo Nkhondo? Nsanja ya Olonda, 10/1/2009

Kodi N’chiyani Chinayambitsa Nkhondo ya Padziko Lonse? Galamukani!, 8/2009

❐ Nsanja ya Olonda, 1/1/2004

Nkhondo Yasintha Masiku Ano

Nkhondo Idzatha

Zida Zopha Mwachinsinsi​—Kodi Zingasakazedi Anthu? Galamukani!, 10/8/2002

Zaka 100 Zachiwawa Galamukani!, 5/8/2002

❐ Galamukani!, 4/8/2001

Mmene Nkhondo Zamasiku Ano Zilili

Zida Zazing’ono Koma Mavuto Aakulu

Kodi Zoletsa Zida Zitha Bwanji M’tsogolo Muno?

❐ Nsanja ya Olonda, 1/1/2001

Mabala a Nkhondo

Kuchiritsa Mabala a Nkhondo

Nkhondo ya Mabomba a Nyukiliya

Zimene Anthu Ambiri Amaopa (Kamutu: Mayiko akhoza kuyambitsa nkhondo ya mabomba anyukiliya nthawi ina iliyonse) Nsanja ya Olonda, 8/1/2010

❐ Galamukani!, 3/8/2004

Kodi Nkhondo ya Nyukiliya Anthu Akuiopabe?

Kodi Nkhondo ya Nyukiliya Angaichititse Ndani?

Kodi Nkhondo ya Nyukiliya Anthu Angaipewe?

Nkhani Zokhudza Chikhalidwe cha Anthu

❐ Galamukani!, 7/2013

Kodi Zionetsero Zimathetsadi Mavuto M’dziko?

Ndinaona Kuti Padzikoli Palibe Chilungamo

❐ Nsanja ya Olonda, 9/1/2012

Mavuto Amene Akazi Amakumana Nawo

Kodi Mulungu Amaona Kuti Akazi Ndi Otsika?

Mulungu Amafuna Kuti Akazi Azilemekezedwa

Kuthandiza Ovutika

Zimene Baibulo Limanena: Anthu Ovutika Galamukani!, 2/2013

Kodi Mphatso Zachifundo Zingathetse Mavuto Athu Onse? Galamukani!, 5/2008

❐ Nsanja ya Olonda, 6/1/2003

Kodi N’chiyani Chikuchitika pa Nkhani Yothandiza Osowa?

Kupatsa Kumene Kumasangalatsa Mulungu

Ukapolo Komanso Kugwiritsa Ana Ntchito Zoposa Msinkhu Wawo

Akapolo Anapeza Ufulu M’mbuyomu Komanso Masiku Ano Nsanja ya Olonda (Yogawira), Na. 2 2017

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Baibulo Limalimbikitsa Ukapolo? Galamukani!, 7/2011

Njira Yomwe Akapolo Ankadutsa Galamukani!, 5/2011

Akapolo Oiwalidwa a ku South Pacific Galamukani!, 1/2009

❐ Galamukani!, 7/8/2002

Ukapolo Ndi Khalidwe Lankhanza Lomwe Lidakalipobe

Tinayamba Kalekale Kulimbana Ndi Ukapolo

Nthawi Imene Ukapolo Udzathe!

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Mulungu Ankakondwera ndi Malonda a Ukapolo? Galamukani!, 9/8/2001

❐ Galamukani!, 3/8/2000

Chinsinsi Chosaululidwa

Kodi Ndani Ali Akapolo Lerolino?

Ukapolo Wamakono Uli Pafupi Kutha!

Tsankho

Zimene Baibulo Limanena: Kusankhana Mitundu Galamukani!, 4/2014

❐ Nsanja ya Olonda, 6/1/2013

Tsankho Likuchitika Padziko Lonse

Kodi Tsankho Lidzatha Liti?

Anthufe Ndi Amodzi Galamukani!, 11/2009

❐ Galamukani!, 8/2009

N’chifukwa Chiyani Anthu Amasankhana?

Kodi Tsankho Limayamba Bwanji?

Chikondi Chimathetsa Tsankho

Kodi Mumaona Anthu Mmene Yehova Amawaonera? Nsanja ya Olonda, 3/15/2008

❐ Galamukani!, 9/8/2004

Zimene Zimayambitsa Tsankho

Mapeto a Tsankho

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Kudana ndi Anthu Amitundu ina N’koyenera? Galamukani!, 8/8/2003

Phunziro la Kukhala Wokoma Mtima Mphunzitsi Waluso, mutu 15

❐ Nsanja ya Olonda, 1/1/2002

Nkhani Yosautsa ya Kusiyana kwa Magulu a Anthu

Kodi N’zothekadi Kuti Anthu Azikhala Mofanana?

Ufulu Wobadwa Nawo

❐ Galamukani!, 5/2012

Zimapweteka Ukamachitiridwa Zopanda Chilungamo

N’chifukwa Chiyani Anthu Amachita Zopanda Chilungamo?

Tingatani Kuti Tizichitira Ena Zachilungamo?

Boma la Mulungu Lidzabweretsa Chilungamo Chenicheni

Anthu Ozunzidwa Apatsidwa Ufulu Nsanja ya Olonda, 3/1/2008

N’zotheka Kupirira Zinthu Zopanda Chilungamo Nsanja ya Olonda, 8/15/2007

❐ Nsanja ya Olonda, 8/1/2006

Anthu Nthawi Zambiri Amachotserana Ulemu

N’zotheka Aliyense Kumadzapatsidwa Ulemu

Mdulidwe wa Akazi

Amayi Akuthana ndi Mavutowa (Kamutu: Kukana Kutsatira Miyambo Yoipa) Galamukani!, 3/8/2005

Kusamukira ku Dziko Lina

Kodi Tingathandize Bwanji Ana a Anthu Ochokera M’mayiko Ena? Nsanja ya Olonda (Yophunzira), 5/2017

❐ Nsanja ya Olonda, 4/15/2014

Simungatumikire Ambuye Awiri

Limbani Mtima, Yehova Akuthandizani

Kodi Osamukira Kudziko Lina Amakapezadi Zimene Akufuna? Galamukani!, 2/2013

Anthu Othawa Kwawo

Tizithandiza Alendo Kuti ‘Azitumikira Yehova Mokondwera’ Nsanja ya Olonda (Yophunzira), 5/2017

❐ Galamukani!, 2/8/2002

Anthu Amene Akufunafuna Bata

Kupeza Malo Amene Angamati Ndiye Kwawo

Dziko Limene Aliyense Angaloledwe Kudzakhalamo

Chiwerengero cha Anthu Padziko Lonse

Vuto Lopezera Chakudya Anthu Okhala M’mizinda Galamukani!, 12/8/2005

Nkhani ya Chiwerengero cha Anthu, M’Baibulo, ndi M’tsogolo Galamukani!, 5/8/2004

Umphawi

Zimene Baibulo Limanena: Umphawi Galamukani!, 9/2015

❐ Nsanja ya Olonda, 6/1/2011

Anthu Ena Ali pa Umphawi Wadzaoneni

Zimene Ena Achita Pofuna Kuthetsa Umphawi

N’chifukwa Chiyani Ambiri Ali Osauka M’dziko Lolemerali? Galamukani!, 5/2007

❐ Nsanja ya Olonda, 5/1/2006

Umphawi Masiku Ano

Tsanzirani Yesu Poganizira Osauka

Kusiyana Kwakukulu Pakati pa Olemera ndi Osauka Galamukani!, 11/8/2005

Kuyesera Kudyetsa Anthu Wani Biliyoni Galamukani!, 8/8/2005

❐ Nsanja ya Olonda, 5/15/2005

Kodi Anthu Angathetse Umphawi?

Dziko Lopanda Umphawi Layandikira

❐ Nsanja ya Olonda, 8/1/2003

Osauka Akusaukirasaukirabe

Kupeza Njira Yothetseratu Umphawi

Kusiyana Pakati pa Olemera ndi Osauka Kukukula Galamukani!, 2/8/2000

Kusowa Pokhala

Umphawi Komanso Vuto Losowa Pokhala Zidzatha Galamukani!, 5/2015

❐ Galamukani!, 12/8/2005

Kusowa Pokhala Ndi Vuto la Padziko Lonse

Kodi N’chiyani Chimayambitsa Vuto la Kusowa Pokhala?

Kodi Kusowa Pokhala Kungathe Bwanji?

❐ Galamukani!, 10/8/2005

Aliyense Amafuna Atakhala ndi Nyumba

Kodi N’chiyani Chimachititsa Vuto la Kusowa kwa Nyumba?

Nyumba Zabwino kwa Aliyense Pomalizira Pake

Zamalonda

Onaninso mutu wakuti Dziko la Satana ➤ Mzimu wa Dziko ➤ Kukonda Chuma

Muzifunafuna Chuma Chenicheni Nsanja ya Olonda (Yophunzira), 7/2017

Chinyengo cha Otsatsa Malonda Galamukani!, 12/2008

“Ntchito Imene Anthu Ambiri Amagwira Padziko Lonse” Galamukani!, 9/8/2005

❐ Galamukani!, 6/8/2002

Kudalirana kwa Mayiko N’kolimbikitsa Komanso N’kokayikitsa

Kodi Kudalirana kwa Mayiko Kungathetsedi Mavuto Athu?

Kudalirana kwa Mayiko Kumene Kudzakupindulitseni

Zokhudza Zachilengedwe

Zimene Muyenera Kudziwa Zokhudza Magetsi ndi Mafuta Galamukani!, Na. 5 2017

Kodi Anthu Apitiriza Kuwononga Dzikoli N’kufika Poti Silingakonzedwenso? Nsanja ya Olonda, 9/1/2014

Kodi Zokambirana Zokhudza Kusokonekera kwa Nyengo Zikuthandiza? Galamukani!, 11/2011

Kodi Matenda a Dzikoli Ndi Ochiritsika? Nsanja ya Olonda, 9/1/2008

❐ Galamukani!, 8/2008

Kodi N’chiyambi cha Mavuto?

Kodi Dziko Lapansi Lili pa Mavuto Aakulu?

Kodi Tsogolo la Dzikoli Lili M’manja mwa Ndani?

Zimene Baibulo Limanena: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusamalira Chilengedwe? Galamukani!, 12/2007

❐ Galamukani!, 4/8/2005

N’chifukwa Chiyani Mapiri Ali Ofunika kwa Ife?

Mapiri Ali Pangozi

Kodi Ndani Adzapulumutse Mapiri?

❐ Galamukani!, 3/8/2005

N’chifukwa Chiyani Mphamvu za Magetsi Zili Zofunika Kwambiri pa Moyo Wathu?

N’chifukwa Chiyani Tikufunika Njira Zatsopano Zopangira Magetsi?

Kodi Pali Njira Zatsopano Zotani Zopangira Magetsi?

Kupeza Gwero la Mphamvu Zonse

Zinthu Zachilengedwe Zikutha Padziko Pano Galamukani!, 1/8/2005

Kodi Zatiyendera Bwanji Pankhani Yoteteza Chilengedwe? Galamukani!, 12/8/2003

Kodi Chikuchitika N’chiyani ndi Nyengoyi? Galamukani!, 8/8/2003

Kodi Chakudya Chathu Tikuchitani? Galamukani!, 1/8/2002

Zachilengedwe Zimadalirana M’njira Zovuta Kuzimvetsa Galamukani!, 12/8/2001

Madzi

❐ Galamukani!, 1/2009

Kodi Madzi Akutha Padzikoli?

Zimene Anthu Akuchita Pofuna kuthetsa Vuto la Kusowa kwa Madzi

Madzi Opatsa Moyo

❐ Galamukani!, 7/8/2001

Kodi Padzikoli Madzi Akutha?

Kodi Madzi Onse Aja Amka Kuti?

Kufufuza Madzi Amoyo

Zomera

❐ Galamukani!, 7/8/2003

Kodi Nkhalango Zachilengedwe za M’madera Otentha Zingatheke Kutetezedwa?

Kodi M’nkhalangozi Tingadulemo Mitengo Mosawononga?

Kodi Nkhalangozi Angaziteteze Ndani?

Mitundu Yosiyanasiyana ya Zinthu N’njofunika M’moyo Galamukani!, 10/8/2001

Kodi Anthu Akudziwonongera Okha Chakudya? Galamukani!, 10/8/2001

Ngozi Zadzidzidzi

Onaninso pamutu wakuti Mboni za Yehova ➤ Kukonzekera Ngozi Zadzidzidzi ndi Kupereka Thandizo

Zimene Tingachite Kuti Tipulumuke Pakachitika Ngozi Zadzidzidzi Galamukani!, Na. 5 2017

Katundu Wanu Yense Atawonongeka Galamukani!, 7/2014

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Mulungu Amalanga Anthu Pogwiritsa Ntchito Masoka Achilengedwe? Galamukani!, 12/2012

❐ Nsanja ya Olonda, 12/1/2011

Kodi Mulungu Akutilanga?

N’chifukwa Chiyani Masoka Achilengedwe Achuluka Chonchi?

Zimene Mungachite Kuti Musavutike Kwambiri ndi Masoka Achilengedwe

Masoka Achilengedwe Adzatha

Tiyembekezere Zivomezi Zinanso Zikuluzikulu Galamukani!, 12/2010

Zimene Owerenga Amafunsa: Kodi Masoka Achilengedwe Ndi Chilango Chochokera kwa Mulungu? Nsanja ya Olonda, 5/1/2008

❐ Galamukani!, 9/2007

N’zothetsa Nzeru Ndiponso Zowononga Chikhulupiriro

Kodi Mulungu Ndiye Amawachititsa?

Masoka Atha Posachedwapa

❐ Galamukani!, 8/8/2005

Kodi Masoka Achilengedwe Akuwonjezeka?

Mmene Zochita za Anthu Zikuwonjezera Masoka Achilengedwe

Masoka Onse Adzatha Posachedwapa

Mzimu wa Dziko

Pewani “Mzimu wa Dziko” Nsanja ya Olonda, 9/15/2008

Woipitsa Zinthu Waonekera Ng’amba! Nsanja ya Olonda, 6/1/2007

Kanizani Mzimu wa Dziko Lomwe Likusinthali Nsanja ya Olonda, 4/1/2004

Kuwonjezeka kwa Makhalidwe Oipa

Tizitsatira Mfundo za Makhalidwe Abwino za Yehova Utumiki Komanso Moyo Wathu, 6/2017

❐ Nsanja ya Olonda, 6/1/2010

Kodi Tasiya Kuopa Tchimo?

Kodi Chasintha N’chiyani pa Nkhani ya Tchimo?

Dziwani Zoona Zake pa Nkhani ya Tchimo

❐ Galamukani!, 4/2007

Nthawi Imene Makhalidwe Analowa Pansi Kwambiri

Kodi Dzikoli Likulowera Kuti?

Kodi Anthu Akusiya Kutsatira Mfundo Zabwino? Galamukani!, 6/8/2003

Kodi Makhalidwe Lerolino N’ngoipirako Kuposa Kale? Galamukani!, 4/8/2000

Kukonda Chuma

Onaninso mutu wakuti Ntchito ndi Ndalama

Zimene Baibulo Limanena: Ndalama Galamukani!, 3/2014

Zinthu Zitatu Zimene Sitingagule ndi Ndalama Galamukani!, 10/2013

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Kudzionetsera Kuli ndi Phindu Lililonse? Galamukani!, 11/2012

Musasunthike Popewa Misampha ya Satana (Kamutu: Msampha wa Kukonda Chuma) Nsanja ya Olonda, 8/15/2012

Musasiye Okhulupirira Anzanu Nsanja ya Olonda, 3/15/2011

Khalani Okhulupirika ndi Mtima Wonse Nsanja ya Olonda, 8/15/2008

Kodi Ndinu “Wolemera kwa Mulungu”? Nsanja ya Olonda, 8/1/2007

❐ Galamukani!, 6/2007

Kodi Moyo Wofunitsitsa Kulemera Ungakusokonezeni Motani?

Kodi Mukufunitsitsa Kukhala Wolemera Mwauzimu?

❐ Nsanja ya Olonda, 2/1/2006

Phunziro pa Nkhani ya Chuma ndi Khalidwe

Chuma Chenicheni Chidzakhala M’dziko Latsopano la Mulungu

❐ Nsanja ya Olonda, 10/15/2004

Kusakasaka Chuma

Pindulani Polimbikira Kuchita Zinthu Zauzimu

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Kukonda Chuma N’kutani Makamaka? Galamukani!, 4/8/2003

Kodi Ndalama Tingazione Motani M’njira Yoyenera? Nsanja ya Olonda, 6/15/2001

Mmene Anthu a M’dzikoli Amaganizira Ndiponso Nzeru za Anthu

Pewani Kutengera Maganizo a M’dzikoli Nsanja ya Olonda (Yophunzira), 11/2017

Ganizani Bwino Kuti Muchite Zinthu Mwanzeru Nsanja ya Olonda, 7/15/2003

Kuphunzirapo Kanthu kwa Akhristu a M’zaka 100 Zoyambirira za Nyengo Yathu Ino Galamukani!, 8/8/2002

Kodi Muyenera Kuwakhulupirira? Nsanja ya Olonda, 12/1/2000

Kodi Mwasonkhezeredwa ndi Anthu Osuliza? Nsanja ya Olonda, 7/15/2000

Chirikizani Chiphunzitso Chaumulungu Molimbika Nsanja ya Olonda, 5/1/2000

Zizolowezi Zoipa

Onaninso mutu wakuti Chiwerewere ➤ Kuonera Zolaula

Mulungu Amakonda Anthu Oyera (Kamutu: Tizipewa Makhalidwe Onse Odetsa) ‘Mulungu Apitirize Kukukondani,’ mutu 8

Sukulu Yamkaka Yopanda Zoseweretsa Galamukani!, 10/8/2004

Nthawi Imene Ukapolo Udzathe! (Kamutu: Zizolowezi Zovuta Kusiya Zikam’sandutsa Munthu Kapolo) Galamukani!, 7/8/2002

Foni, TV, Kompyuta ndi Intaneti

Musamagwiritse Ntchito Zipangizo Zamakono Monyanyira Galamukani!, 4/2015

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndimagwiritsira Ntchito Foni, TV, Kompyuta Kapena Intaneti Mopitirira Malire? Galamukani!, 1/2011

Kodi Ndimagwiritsa Ntchito Zipangizo Zamakono Mopitirira Muyezo? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 36

Zochitika Padzikoli (Kamutu: Kodi Mungakodwe ndi Masewera a Pakompyuta?) Galamukani!, 4/2007

Mowa

Kodi Kumwa Mowa Wambiri Kuli ndi Vuto Lanji? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 34

❐ Nsanja ya Olonda, 1/1/2010

“Ndingomwako Botolo Limodzi Lokha”

Maganizo a Mulungu pa Nkhani ya Kumwa Mowa

Khalani ndi Maganizo Oyenera pa Nkhani ya Kumwa Mowa

Ndingatani Makolo Anga Akamaledzera Kapena Kumwa Mankhwala Osokoneza Bongo? Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 23

Sindinenso Kapolo wa Mowa Galamukani!, 5/2007

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Kumwa Mowa N’kulakwa? Galamukani!, 12/2006

❐ Galamukani!, 10/8/2005

Mmene Kumwa Mowa Mopitirira Muyeso Kumakhudzira Thanzi la Munthu

Kupulumuka ku Msampha wa Kumwa Mowa Mopitirira Muyeso

Mowa Umafunika Kusamala Nawo Nsanja ya Olonda, 12/1/2004

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Kumwa Mowa Mwauchidakwa N’koipadi? Galamukani!, 3/8/2004

Mukhoza Kulaka Mavuto Owononga Banja (Kamutu: Kuwononga kwa Uchidakwa; Kamutu: Kodi Banja Lingachitenji?) Chinsinsi cha Banja, mutu 12

Mankhwala

Kodi Ndingatani Kuti Ndisiye Kugwiritsa Ntchito Mankhwala Osokoneza Bongo? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 35

❐ Galamukani!, 5/2009

Anthu Akumwa Mankhwala Mwachisawawa

Kugwiritsa Ntchito Mankhwala Koyenera ndi Kosayenera

Njira Yabwino Yothetsera Vuto Logwiritsa Ntchito Mankhwala Mwachisawawa

Ndingatani Makolo Anga Akamaledzera Kapena Kumwa Mankhwala Osokoneza Bongo? Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 23

❐ Galamukani!, 4/8/2003

Mankhwala Osokoneza Bongo Pakati pa Achinyamata

Mmene Mungatetezere Ana Anu

Vuto la Mankhwalawa Litha Posachedwapa Padziko Lonse

❐ Galamukani!, 7/8/2001

Kodi Ndani Amagwiritsa Ntchito Mankhwala Osokoneza Bongo?

N’chifukwa Chiyani Anthu Amagwiritsa Ntchito Mankhwala Osokoneza Bongo?

Vuto la Mankhwala Osokoneza Bongo Lingathetsedwe!

Fodya

❐ Nsanja ya Olonda, 6/1/2014

Mliri wa Padziko Lonse

Kodi Mawu a Mulungu Amati Chiyani pa Nkhani ya Kusuta Fodya?

Zimene Owerenga Amafunsa: Kodi Mulungu Amaona Kuti N’kulakwa Kusuta Fodya? Nsanja ya Olonda, 8/1/2012

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndiyenera Kudziwa Chiyani Zokhudza Kusuta Fodya? Galamukani!, 3/2011

Kodi Mumadziwa Zotani pa Nkhani ya Fodya? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 33

❐ Galamukani!, 5/2010

Chikondi cha Mpeni Kumphasa

Khalani Wotsimikiza

Pemphani Thandizo

Konzekerani Kukumana ndi Mavuto

N’zotheka Kusiya Fodya

Kutsogoleredwa ndi Nzeru Zapamwamba Kuposa Zachibadwa (Kamutu: “Pemphanibe” Mulungu Kuti Akuthandizeni) Galamukani!, 7/2007

Mtedza wa Betel

Muziona Moyo Ngati Mmene Mulungu Amauonera Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, mutu 13 ¶7

Muziona Kuti Moyo Ndi Mphatso Yamtengo Wapatali Zimene Baibulo Limaphunzitsa, mutu 13 ¶6-7

Kodi Kudya Mtedza wa Betel Kuli ndi Mavuto Otani? Galamukani!, 2/2012

Anthu Ovomerezeka ndi Mulungu Adzapeza Moyo Wosatha Nsanja ya Olonda, 2/15/2011 ¶12

Kutchova Juga

Zimene Baibulo Limanena: Kutchova Juga Galamukani!, 3/2015

Kodi Baibulo Limaletsa Kutchova Juga? Nsanja ya Olonda, 3/1/2011

Mafunso Ochokera kwa Owerenga: Kodi sikulakwa kutchova njuga ngati ndalama zobetcherana n’zochepa chabe? Nsanja ya Olonda, 11/1/2002

❐ Galamukani!, 8/8/2002

Kutchova Njuga Kwatenga Malo Padziko Lonse

Kodi Kutchova Njuga Kuli Ndi Vuto Lanji?

Pewani Msampha wa Kutchova Njuga

Njira Zoperekera Mauthenga

Tetezani Maganizo Anu Nsanja ya Olonda (Yophunzira), 7/2017

Kodi Ofalitsa Nkhani Tingawakhulupirire? Galamukani!, 12/2013

❐ Galamukani!, 11/8/2005

Mphamvu Zimene Manyuzipepala Ali Nazo

Kuuza Anthu Nkhani

Mmene Mungapindulire ndi Manyuzipepala

❐ Galamukani!, 7/8/2000

Nkhani Zokopa Zingaphetse Anthu

Kupotoza Nkhani

Musanyengedwe ndi Nkhani Zokopa!

Aramagedo

Onani pamutu wakuti Baibulo ➤ Ulosi ➤ Chisautso Chachikulu Komanso Aramagedo

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena