Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsamba 2
  • “Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso ndi Moyo?”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso ndi Moyo?”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Yehova Anagwiritsa Ntchito Akazi Awiri Populumutsa Anthu Ake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Tizitamanda Yehova Chifukwa ndi Wanzeru
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 November tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso ndi Moyo?”

Anthu alibe mphamvu zolepheretsa imfa kapena kubwezeretsa moyo (Yob 14:​1, 2, 4, 10; w99 10/15 3 ¶1-3)

Anthu omwe anamwalira angakhalenso ndi moyo (Yob 14:​7-9; w15 4/15 32 ¶1-2)

Yehova amalakalaka kudzaukitsa atumiki ake omwe anamwalira, ndipo ali ndi mphamvu zochitira zimenezi (Yob 14: 14, 15; w11 3/1 22 ¶5)

Zithunzi: 1. Chitsa cha mtengo chikuphuka. 2. Mayi akukumbatira mwana wake amene waukitsidwa m’Paradaiso.

MAFUNSO OFUNIKA KUWAGANIZIRA: N’chifukwa chiyani Yehova amalakalaka kudzaukitsa atumiki ake okhulupirika? Mukaganizira zimenezi, kodi mukuona kuti Yehova ndi wotani?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena