8 Chotero si inu amene munanditumiza kuno,+ koma Mulungu woona. Anachita zimenezi kuti andiike kukhala tate+ kwa Farao, ndi mbuye wa nyumba yake yonse, ndiponso woyang’anira wa dziko lonse la Iguputo.
10 ndipo anamulanditsa m’masautso ake onse. Anamupatsanso chisomo ndi nzeru pamaso pa Farao mfumu ya Iguputo. Ndipo anamuika kuti ayang’anire Iguputo ndi nyumba yonse ya Farao.+